Oweruza 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ankabwera nʼkuwawonongera zokolola zawo zonse mpaka kukafika ku Gaza. Sankawasiyira chakudya chilichonse ngakhalenso nkhosa, ngʼombe kapena bulu.+
4 Ankabwera nʼkuwawonongera zokolola zawo zonse mpaka kukafika ku Gaza. Sankawasiyira chakudya chilichonse ngakhalenso nkhosa, ngʼombe kapena bulu.+