-
Deuteronomo 28:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Ngʼombe yanu idzaphedwa inu mukuona, koma simudzadya nyama yake. Bulu wanu adzabedwa inu mukuona ndipo simudzamuonanso. Nkhosa yanu idzaperekedwa kwa adani anu ndipo sipadzakhala wokupulumutsani.
-