Nehemiya 9:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Mafumu amene mwalola kuti azitilamulira chifukwa cha machimo athu+ ndi amene akusangalala ndi zokolola zochuluka zamʼdzikoli. Iwo akulamulira matupi athu komanso ziweto zathu mmene akufunira, ndipo tili pamavuto aakulu. Yesaya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dziko lanu lawonongedwa. Mizinda yanu yawotchedwa ndi moto. Alendo akudya zokolola zochokera munthaka yanu, inu mukuona.+ Lawonongedwa ngati dziko limene lalandidwa ndi adani.+
37 Mafumu amene mwalola kuti azitilamulira chifukwa cha machimo athu+ ndi amene akusangalala ndi zokolola zochuluka zamʼdzikoli. Iwo akulamulira matupi athu komanso ziweto zathu mmene akufunira, ndipo tili pamavuto aakulu.
7 Dziko lanu lawonongedwa. Mizinda yanu yawotchedwa ndi moto. Alendo akudya zokolola zochokera munthaka yanu, inu mukuona.+ Lawonongedwa ngati dziko limene lalandidwa ndi adani.+