Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+ Deuteronomo 28:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Anthu amene simukuwadziwa adzadya zipatso zamʼdziko lanu ndi mbewu zanu zonse+ ndipo nthawi zonse muzidzaberedwa mwachinyengo komanso kuponderezedwa. Nehemiya 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Enanso ankanena kuti: “Ife takongola ndalama kuti tikhome msonkho kwa mfumu wa minda yathu ya tirigu ndi ya mpesa.+
15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+
33 Anthu amene simukuwadziwa adzadya zipatso zamʼdziko lanu ndi mbewu zanu zonse+ ndipo nthawi zonse muzidzaberedwa mwachinyengo komanso kuponderezedwa.
4 Enanso ankanena kuti: “Ife takongola ndalama kuti tikhome msonkho kwa mfumu wa minda yathu ya tirigu ndi ya mpesa.+