Genesis 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Pa chiyambi,+ Mulungu+ analenga+ kumwamba ndi dziko lapansi.+ Salimo 146:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi,+Nyanja ndi zonse zili mmenemo.+Wosunga choonadi mpaka kalekale.+ Chivumbulutso 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+
6 Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi,+Nyanja ndi zonse zili mmenemo.+Wosunga choonadi mpaka kalekale.+ Chivumbulutso 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+
11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+