Deuteronomo 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo iwe ukudziwa bwino kuti Yehova Mulungu wako ndi Mulungu woona,+ Mulungu wokhulupirika,+ wosunga pangano+ ndiponso wosonyeza kukoma mtima kosatha kwa anthu amene amam’konda ndi kusunga malamulo ake ku mibadwo masauzande,+ Salimo 71:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inenso ndidzakutamandani ndi chipangizo cha zingwe,+Ndidzatamanda choonadi chanu, inu Mulungu.+Ndidzaimba nyimbo zokutamandani ndi zeze, Inu Woyera wa Isiraeli.+
9 Ndipo iwe ukudziwa bwino kuti Yehova Mulungu wako ndi Mulungu woona,+ Mulungu wokhulupirika,+ wosunga pangano+ ndiponso wosonyeza kukoma mtima kosatha kwa anthu amene amam’konda ndi kusunga malamulo ake ku mibadwo masauzande,+
22 Inenso ndidzakutamandani ndi chipangizo cha zingwe,+Ndidzatamanda choonadi chanu, inu Mulungu.+Ndidzaimba nyimbo zokutamandani ndi zeze, Inu Woyera wa Isiraeli.+