Salimo 92:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo ndidzatero pogwiritsa ntchito choimbira cha zingwe 10 ndi choimbira cha zingwe zitatu.+Ndidzaimba nyimbo yomveka bwino ndi zeze.+ Salimo 150:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mutamandeni mwa kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa.+Mutamandeni ndi choimbira cha zingwe ndi zeze.+
3 Ndipo ndidzatero pogwiritsa ntchito choimbira cha zingwe 10 ndi choimbira cha zingwe zitatu.+Ndidzaimba nyimbo yomveka bwino ndi zeze.+
3 Mutamandeni mwa kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa.+Mutamandeni ndi choimbira cha zingwe ndi zeze.+