Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 14:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano Asa anayamba kupemphera kwa Yehova Mulungu wake,+ kuti: “Inu Yehova mukafuna kuthandiza, zilibe kanthu kuti anthuwo ndi ambiri kapena ndi opanda mphamvu.+ Tithandizeni Yehova Mulungu wathu chifukwa tikudalira inu,+ ndipo tabwera m’dzina lanu+ kudzamenyana ndi khamuli. Inu Yehova ndinu Mulungu wathu.+ Musalole kuti munthu akuposeni mphamvu.”+

  • 2 Mbiri 20:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Inu Mulungu wathu kodi simuwaweruza?+ Ifeyo patokha tilibe mphamvu zotha kulimbana ndi khamu lalikulu limene likubwera kudzamenyana nafeli+ ndipo sitikudziwa chochita,+ koma maso athu ali pa inu.”+

  • 2 Mbiri 32:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Iyo ikudalira mphamvu za anthu,*+ koma ife tili ndi Yehova Mulungu wathu+ kuti atithandize ndi kutimenyera nkhondo zathu.”+ Pamenepo anthuwo anayamba kulimba mtima chifukwa cha mawu a Hezekiya mfumu ya Yuda.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena