Deuteronomo 32:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ndidzalengeza dzina la Yehova.+Vomerezani ukulu wa Mulungu wathu!+ Maliko 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yesu anayankha kuti: “Loyamba n’lakuti, ‘Tamverani Aisiraeli inu, Yehova* Mulungu wathu ndi Yehova mmodzi.+
29 Yesu anayankha kuti: “Loyamba n’lakuti, ‘Tamverani Aisiraeli inu, Yehova* Mulungu wathu ndi Yehova mmodzi.+