Salimo 34:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndidzatamanda Yehova nthawi zonse.+Ndidzamutamanda ndi pakamwa panga mosalekeza.+ Salimo 103:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 103 Tamanda Yehova, iwe moyo wanga.+Chilichonse mkati mwanga, chitamande dzina lake loyera.+