Deuteronomo 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Yehova Mulungu wako akadzawononga mitundu+ ya m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, iwe n’kuwalandadi dzikolo ndi kukhala m’mizinda yawo ndi m’nyumba zawo,+
19 “Yehova Mulungu wako akadzawononga mitundu+ ya m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, iwe n’kuwalandadi dzikolo ndi kukhala m’mizinda yawo ndi m’nyumba zawo,+