Salimo 95:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 95 Bwerani tifuule kwa Yehova mokondwera!+Iye amene ndi Thanthwe la chipulumutso chathu, timufuulire mosangalala chifukwa wapambana.+
95 Bwerani tifuule kwa Yehova mokondwera!+Iye amene ndi Thanthwe la chipulumutso chathu, timufuulire mosangalala chifukwa wapambana.+