Salimo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.] Miyambo 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Woipa adzagwidwa ndi zolakwa zake zomwe,+ ndipo adzamangidwa m’zingwe za tchimo lake lomwe.+
16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.]