Miyambo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akamanena kuti: “Tiye tipitire limodzi. Tiye tikabisalire anthu kuti tikakhetse magazi.+ Tiye tikabisalire anthu osalakwa. Tikachite zimenezo popanda chifukwa chilichonse.+ Miyambo 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa mapazi awo amathamangira zoipa,+ ndipo iwo amafulumira kukakhetsa magazi.+ Yesaya 59:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mapazi awo amangothamangira kukachita zoipa,+ ndipo amafulumira kuti akakhetse magazi osalakwa.+ Maganizo awo ndi opweteka anzawo.+ M’misewu mwawo amangokhalira kusakazana ndi kuwonongana.+ Aroma 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Mapazi awo amathamangira kukhetsa magazi.”+
11 Akamanena kuti: “Tiye tipitire limodzi. Tiye tikabisalire anthu kuti tikakhetse magazi.+ Tiye tikabisalire anthu osalakwa. Tikachite zimenezo popanda chifukwa chilichonse.+
7 Mapazi awo amangothamangira kukachita zoipa,+ ndipo amafulumira kuti akakhetse magazi osalakwa.+ Maganizo awo ndi opweteka anzawo.+ M’misewu mwawo amangokhalira kusakazana ndi kuwonongana.+