Yeremiya 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu anga ndi opusa.+ Iwo sanaganizire za ine.+ Iwo ndi ana opanda nzeru ndipo sazindikira kalikonse.+ Iwo ndi anzeru pa kuchita zoipa koma sadziwa kuchita zabwino.+ Mika 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu mumadana ndi zinthu zabwino+ ndi kukonda zinthu zoipa.+ Mumasenda khungu la anthu ndi kuchotsa mnofu pamafupa awo.+
22 Anthu anga ndi opusa.+ Iwo sanaganizire za ine.+ Iwo ndi ana opanda nzeru ndipo sazindikira kalikonse.+ Iwo ndi anzeru pa kuchita zoipa koma sadziwa kuchita zabwino.+
2 Inu mumadana ndi zinthu zabwino+ ndi kukonda zinthu zoipa.+ Mumasenda khungu la anthu ndi kuchotsa mnofu pamafupa awo.+