Yohane 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chakudya chamadzulo chili mkati, Mdyerekezi anali ataika kale maganizo ofuna kupereka Yesu+ mumtima mwa Yudasi Isikariyoti,+ mwana wa Simoni.
2 Chakudya chamadzulo chili mkati, Mdyerekezi anali ataika kale maganizo ofuna kupereka Yesu+ mumtima mwa Yudasi Isikariyoti,+ mwana wa Simoni.