Yeremiya 48:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Tamva za kunyada kwa Mowabu. Iye ndi wodzikuza kwambiri.Tamva za kudzitukumula kwake, kunyada kwake, kudzikweza kwake ndi kudzikuza kwa mtima wake.”+
29 “Tamva za kunyada kwa Mowabu. Iye ndi wodzikuza kwambiri.Tamva za kudzitukumula kwake, kunyada kwake, kudzikweza kwake ndi kudzikuza kwa mtima wake.”+