Yesaya 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngakhale munthu woipa atachitiridwa zabwino, sangaphunzire chilungamo.+ M’dziko lochita zowongoka, iye adzachita zinthu zopanda chilungamo+ ndipo sadzaona ukulu wa Yehova.+ Yeremiya 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma pambuyo pake, iwo anatembenuka+ ndi kuyamba kutenganso amuna ndi akazi antchitowo amene anawalola kupita kwawo mwaufulu ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito monga antchito awo aamuna ndi aakazi.+
10 Ngakhale munthu woipa atachitiridwa zabwino, sangaphunzire chilungamo.+ M’dziko lochita zowongoka, iye adzachita zinthu zopanda chilungamo+ ndipo sadzaona ukulu wa Yehova.+
11 Koma pambuyo pake, iwo anatembenuka+ ndi kuyamba kutenganso amuna ndi akazi antchitowo amene anawalola kupita kwawo mwaufulu ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito monga antchito awo aamuna ndi aakazi.+