Salimo 78:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Iwo anali kubwerera ndi kuchita zinthu mwachinyengo ngati makolo awo.+Anapotoka maganizo ngati uta wosakunga kwambiri.+ Yeremiya 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “M’kupita kwa nthawi, ndinakulowetsani m’dziko la minda ya zipatso kuti mudye zipatso zake ndi zinthu zabwino za m’dzikolo,+ koma munalowa m’dziko langa ndi kuliipitsa. Cholowa changa munachisandutsa chinthu chonyansa.+
57 Iwo anali kubwerera ndi kuchita zinthu mwachinyengo ngati makolo awo.+Anapotoka maganizo ngati uta wosakunga kwambiri.+
7 “M’kupita kwa nthawi, ndinakulowetsani m’dziko la minda ya zipatso kuti mudye zipatso zake ndi zinthu zabwino za m’dzikolo,+ koma munalowa m’dziko langa ndi kuliipitsa. Cholowa changa munachisandutsa chinthu chonyansa.+