Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 13:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Anauza Mose kuti: “Tinakalowa m’dziko limene munatitumako. Ndithudi ndi dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ ndipo zipatso zake ndi izi.+

  • Deuteronomo 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 yokhalanso ndi nyumba zodzaza ndi zinthu zonse zabwino zimene sunaikemo ndiwe, ndi zitsime* zimene sunakumbe ndiwe, minda ya mpesa ndi mitengo ya maolivi imene sunabzale ndiwe, n’kudya ndi kukhuta,+

  • Deuteronomo 8:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pakuti Yehova Mulungu wanu akukulowetsani m’dziko labwino,+ dziko la zigwa* za madzi,+ akasupe ndi madzi ochuluka otuluka m’zigwa ndi m’madera a mapiri,

  • Nehemiya 9:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Iwo analanda mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+ Analandanso nthaka yachonde,+ nyumba zodzaza ndi zinthu zonse zabwino,+ zitsime,*+ minda ya mpesa ndi ya maolivi+ ndi mitengo ya zipatso yochuluka. Atatero, anayamba kudya, kukhuta,+ kunenepa+ ndi kukondwera ndi ubwino wanu waukulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena