Levitiko 25:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Pakuti ana a Isiraeli ndi akapolo anga amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo.+ Asamadzigulitse mmene amadzigulitsira akapolo. Salimo 36:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mawu a pakamwa pake ndi opweteka ndi achinyengo.+Wasiya kugwiritsa ntchito nzeru zomuthandiza kuchita zinthu zabwino.+
42 Pakuti ana a Isiraeli ndi akapolo anga amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo.+ Asamadzigulitse mmene amadzigulitsira akapolo.
3 Mawu a pakamwa pake ndi opweteka ndi achinyengo.+Wasiya kugwiritsa ntchito nzeru zomuthandiza kuchita zinthu zabwino.+