Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 8:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Popeza anthu ochita zoipa sanalangidwe msanga,+ n’chifukwa chake mtima wa ana a anthu wakhazikika pa kuchita zoipa.+

  • Yesaya 56:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Tabwerani amuna inu! Dikirani kaye ndikatenge vinyo. Timwe mpaka kuledzera.+ Mawa lidzakhalanso ngati lero, mwinanso kuposa pamenepa.”+

  • Chivumbulutso 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pa muyezo umene anadzipezera ulemerero ndi kusangalala ndi chuma mopanda manyazi, pa muyezo womwewo mumuzunze ndi kumuliritsa.+ Pakuti mumtima mwake akumanena kuti, ‘Ine ndine mfumukazi.+ Sindine mkazi wamasiye,+ ndipo sindidzalira+ ngakhale pang’ono.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena