Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 31:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 N’kosayenera kwa mafumu iwe Lemueli, n’kosayenera kuti mafumu azimwa vinyo,+ kapena kuti akuluakulu olemekezeka azinena kuti: “Kodi chakumwa choledzeretsa chili kuti?”

  • Yesaya 5:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Tsoka kwa anthu amene ali eni ake omwa vinyo kwambiri, ndi kwa anthu amene ali akatswiri odziwa kusakaniza zakumwa zoledzeretsa.+

  • Yesaya 28:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Amenewanso asochera chifukwa cha vinyo. Akuyenda uku ndi uku chifukwa cha chakumwa choledzeretsa. Ansembe ndi aneneri+ asochera chifukwa cha chakumwa choledzeretsa. Asokonezeka chifukwa cha vinyo. Akuyenda uku ndi uku+ chifukwa cha chakumwa choledzeretsa. Sakuonanso bwino ndipo zochita zawo zikusonyeza kuti sakuganiza bwino.

  • Hoseya 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Dama, vinyo wakale ndi vinyo wotsekemera zimawononga nzeru za munthu.+

  • Mateyu 24:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 n’kuyamba kumenya akapolo anzake ndi kudya komanso kumwa limodzi ndi zidakwa zenizeni,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena