Yesaya 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amenewanso asochera chifukwa cha vinyo.Akuyenda modzandira chifukwa cha mowa. Wansembe ndi mneneri asochera chifukwa cha mowa.Vinyo wawasokoneza,Ndipo akuyenda modzandira chifukwa cha mowa.Sakuona bwinobwino ndipo akusochera,Komanso akulephera kusankha zinthu mwanzeru.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:7 Yesaya 1, ptsa. 289-291, 300-301 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, ptsa. 12-13
7 Amenewanso asochera chifukwa cha vinyo.Akuyenda modzandira chifukwa cha mowa. Wansembe ndi mneneri asochera chifukwa cha mowa.Vinyo wawasokoneza,Ndipo akuyenda modzandira chifukwa cha mowa.Sakuona bwinobwino ndipo akusochera,Komanso akulephera kusankha zinthu mwanzeru.+