Yeremiya 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Aneneri akulosera monama,+ ndipo ansembe akupondereza anthu ndi mphamvu zawo.+ Anthu anga nawonso akukonda zimenezi.+ Ndipo kodi anthu inu mudzachita chiyani pamapeto pake?”+ Yeremiya 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Ndaona zosayenera mwa aneneri a ku Samariya.+ Iwo atumikira ngati aneneri a Baala+ ndipo asocheretsa anthu anga, Aisiraeli.+
31 Aneneri akulosera monama,+ ndipo ansembe akupondereza anthu ndi mphamvu zawo.+ Anthu anga nawonso akukonda zimenezi.+ Ndipo kodi anthu inu mudzachita chiyani pamapeto pake?”+
13 “Ndaona zosayenera mwa aneneri a ku Samariya.+ Iwo atumikira ngati aneneri a Baala+ ndipo asocheretsa anthu anga, Aisiraeli.+