Yeremiya 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Ndaona zinthu zonyansa mwa aneneri a ku Samariya.+ Iwo akulosera mʼdzina la BaalaNdipo akusocheretsa anthu anga, Aisiraeli.
13 “Ndaona zinthu zonyansa mwa aneneri a ku Samariya.+ Iwo akulosera mʼdzina la BaalaNdipo akusocheretsa anthu anga, Aisiraeli.