Miyambo 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Munthu wanzeru amachita mantha ndipo amapatuka pa choipa,+ koma wopusa amapsa mtima ndiponso amakhala wodzidalira.+
16 Munthu wanzeru amachita mantha ndipo amapatuka pa choipa,+ koma wopusa amapsa mtima ndiponso amakhala wodzidalira.+