1 Samueli 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiye ine nditenge mkate wanga,+ madzi ndi nyama imene ndaphera anyamata anga ometa ubweya wa nkhosa n’kupereka kwa amuna amene sindikudziwa m’pang’ono pomwe kumene achokera?”+ 1 Mafumu 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yezebeli atamva zimenezo, anatuma munthu kwa Eliya kuti akamuuze kuti: “Milungu yanga indilange+ mowirikiza,+ ngati pofika nthawi ino mawa sindidzachititsa moyo wako kukhala ngati moyo wa aliyense wa aneneriwo.”
11 Ndiye ine nditenge mkate wanga,+ madzi ndi nyama imene ndaphera anyamata anga ometa ubweya wa nkhosa n’kupereka kwa amuna amene sindikudziwa m’pang’ono pomwe kumene achokera?”+
2 Yezebeli atamva zimenezo, anatuma munthu kwa Eliya kuti akamuuze kuti: “Milungu yanga indilange+ mowirikiza,+ ngati pofika nthawi ino mawa sindidzachititsa moyo wako kukhala ngati moyo wa aliyense wa aneneriwo.”