Deuteronomo 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Samalani kuti munganene mumtima mwanu kuti, ‘Chuma ichi ndachipeza ndi mphamvu zanga ndi nyonga za dzanja langa.’+ Oweruza 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma poyankha, akalonga a ku Sukoti anati: “Tipatsirenji asilikali ako mkate ngati kuti wagwira kale Zeba ndi Zalimuna?”+ 2 Akorinto 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano amene amapereka mbewu kwa wobzala, amenenso amapereka chakudya kuti anthu adye,+ adzakupatsani mbewu zoti mubzale ndipo adzakupatsani zimenezi mowolowa manja. Adzawonjezeranso zipatso za chilungamo chanu.)+
17 Samalani kuti munganene mumtima mwanu kuti, ‘Chuma ichi ndachipeza ndi mphamvu zanga ndi nyonga za dzanja langa.’+
6 Koma poyankha, akalonga a ku Sukoti anati: “Tipatsirenji asilikali ako mkate ngati kuti wagwira kale Zeba ndi Zalimuna?”+
10 Tsopano amene amapereka mbewu kwa wobzala, amenenso amapereka chakudya kuti anthu adye,+ adzakupatsani mbewu zoti mubzale ndipo adzakupatsani zimenezi mowolowa manja. Adzawonjezeranso zipatso za chilungamo chanu.)+