Ezekieli 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Ngati mneneri wapusitsidwa n’kulankhula mawu, ineyo Yehova ndi amene ndamupusitsa mneneriyo.+ Ndidzamutambasulira dzanja langa n’kumuwononga pakati pa anthu anga, Aisiraeli.+ 2 Atesalonika 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ichi n’chifukwa chake Mulungu walola kuti iwo anyengedwe ndipo azikhulupirira bodza,+
9 “‘Ngati mneneri wapusitsidwa n’kulankhula mawu, ineyo Yehova ndi amene ndamupusitsa mneneriyo.+ Ndidzamutambasulira dzanja langa n’kumuwononga pakati pa anthu anga, Aisiraeli.+