Ezekieli 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Koma ngati mneneri wapusitsidwa nʼkupereka yankho, ineyo Yehova ndi amene ndapusitsa mneneriyo.+ Choncho ndidzatambasula dzanja langa nʼkumuwononga kuti asakhalenso pakati pa anthu anga, Aisiraeli.
9 ‘Koma ngati mneneri wapusitsidwa nʼkupereka yankho, ineyo Yehova ndi amene ndapusitsa mneneriyo.+ Choncho ndidzatambasula dzanja langa nʼkumuwononga kuti asakhalenso pakati pa anthu anga, Aisiraeli.