1 Mafumu 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye anayankha kuti, ‘Ndipita kukakhala mzimu wabodza m’kamwa mwa aneneri ake onse.’+ Ndiyeno Mulungu anati, ‘Ukam’pusitsadi ndipo zikakuyendera bwino.+ Pita kachite momwemo.’+ Yeremiya 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo ndinanena kuti: “Kalanga ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Kunena zoona, mwapusitsa anthu awa+ ndiponso Yerusalemu mwa kunena kuti, ‘Mudzakhala pa mtendere,’+ koma lupanga lawabaya* mpaka mumtima.” 2 Atesalonika 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ichi n’chifukwa chake Mulungu walola kuti iwo anyengedwe ndipo azikhulupirira bodza,+
22 Iye anayankha kuti, ‘Ndipita kukakhala mzimu wabodza m’kamwa mwa aneneri ake onse.’+ Ndiyeno Mulungu anati, ‘Ukam’pusitsadi ndipo zikakuyendera bwino.+ Pita kachite momwemo.’+
10 Pamenepo ndinanena kuti: “Kalanga ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Kunena zoona, mwapusitsa anthu awa+ ndiponso Yerusalemu mwa kunena kuti, ‘Mudzakhala pa mtendere,’+ koma lupanga lawabaya* mpaka mumtima.”