Yobu 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma amuna inu ndinu onamizira anzanu.+Nonsenu ndinu madokotala opanda phindu.+ Yeremiya 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo akuyesa kuchiritsa mwachinyengo+ kuwonongeka kwa anthu anga ponena kuti, ‘Kuli mtendere! Kuli mtendere!’ pamene kulibe mtendere.+
14 Iwo akuyesa kuchiritsa mwachinyengo+ kuwonongeka kwa anthu anga ponena kuti, ‘Kuli mtendere! Kuli mtendere!’ pamene kulibe mtendere.+