Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 6:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mofanana ndi zimenezi, amuna inu mwakhala opanda pake,+

      Mwaona zoopsa n’kuyamba kuchita mantha.+

  • Yobu 16:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 “Ndamva zinthu zambiri ngati zimenezi.

      Nonsenu ndinu otonthoza onditopetsa!+

  • Yeremiya 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iwo akuyesa kuchiritsa mwachinyengo+ kuwonongeka kwa anthu anga ponena kuti, ‘Kuli mtendere! Kuli mtendere!’ pamene kulibe mtendere.+

  • Ezekieli 34:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Nkhosa zodwala simunazilimbitse+ ndipo zamatenda simunazichiritse. Yothyoka mwendo simunaimange mwendo wothyokawo. Nkhosa zomwazika simunazibweze ndipo zosochera simunazifufuze kuti muzipeze.+ Munali kuzilamulira mouma mtima komanso mwankhanza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena