Mateyu 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’malomwake, nthawi zonse muzipita kwa nkhosa zosochera za nyumba ya Isiraeli.+ Luka 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ndani wa inu amene atakhala ndi nkhosa 100, imodzi n’kutayika, sangasiye nkhosa 99 zinazo m’chipululu, n’kupita kukafunafuna imodzi yotayikayo kufikira ataipeza?+
4 “Ndani wa inu amene atakhala ndi nkhosa 100, imodzi n’kutayika, sangasiye nkhosa 99 zinazo m’chipululu, n’kupita kukafunafuna imodzi yotayikayo kufikira ataipeza?+