Ezekieli 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inetu ndidzafunafuna nkhosa zanga ndi kuzisamalira.+ Mateyu 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Mukuganiza bwanji? Ngati munthu ali ndi nkhosa 100 ndipo imodzi mwa nkhosazo n’kusochera,+ kodi sangasiye nkhosa 99 zija m’phiri ndi kupita kukafunafuna yosocherayo?+ Luka 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti Mwana wa munthu anabwera kudzafunafuna ndi kupulumutsa anthu osochera.”+ 1 Petulo 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti munali ngati nkhosa zosochera,+ koma tsopano mwabwerera kwa m’busa+ wanu ndi woyang’anira miyoyo yanu.
11 “‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inetu ndidzafunafuna nkhosa zanga ndi kuzisamalira.+
12 “Mukuganiza bwanji? Ngati munthu ali ndi nkhosa 100 ndipo imodzi mwa nkhosazo n’kusochera,+ kodi sangasiye nkhosa 99 zija m’phiri ndi kupita kukafunafuna yosocherayo?+
25 Pakuti munali ngati nkhosa zosochera,+ koma tsopano mwabwerera kwa m’busa+ wanu ndi woyang’anira miyoyo yanu.