-
Zekariya 11:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Pakuti ndilola kuti m’dzikoli mukhale m’busa wina.+ M’busa ameneyu sadzasamala nkhosa zimene zikuwonongeka.+ Nkhosa yaing’ono sadzaifunafuna, ndipo yothyoka sadzaichiritsa.+ Nkhosa yotha kuima yokha sadzaipatsa chakudya, ndipo adzadya nyama ya nkhosa yonenepa.+ Iye adzakupula ziboda za nkhosazo.+
-