Genesis 31:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pa zaka 20 zonsezi zimene ndakhala nanu, nkhosa zanu zazikazi ndi mbuzi zanu zazikazi sizinaberekepo mwana wakufa.+ Ndiponso, chikhalire sindinadyeko ndi imodzi yomwe ya nkhosa zanu zamphongo. Ezekieli 34:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu mukudya mafuta,+ ndipo mukuvala zovala zaubweya wa nkhosa. Mukupha+ nyama zonenepa,+ koma nkhosa simukuzidyetsa.
38 Pa zaka 20 zonsezi zimene ndakhala nanu, nkhosa zanu zazikazi ndi mbuzi zanu zazikazi sizinaberekepo mwana wakufa.+ Ndiponso, chikhalire sindinadyeko ndi imodzi yomwe ya nkhosa zanu zamphongo.
3 Inu mukudya mafuta,+ ndipo mukuvala zovala zaubweya wa nkhosa. Mukupha+ nyama zonenepa,+ koma nkhosa simukuzidyetsa.