Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 23:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Yehova Mulungu wa Isiraeli wadzudzula abusa amene akuweta anthu ake kuti: “Inu mwabalalitsa nkhosa zanga. Mukupitiriza kuzimwaza ndipo simukuzisamalira.”+

      “Tsopano ndikutembenukira kwa inu chifukwa cha zochita zanu zoipazo,”+ watero Yehova.

  • Ezekieli 34:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Nkhosa zanga+ zinasochera m’mapiri onse ndi m’zitunda zonse zitalizitali.+ Zinabalalika padziko lonse lapansi, ndipo panalibe wozifufuza ndi kuziyang’anayang’ana.

  • Mateyu 9:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Poona chikhamu cha anthu, iye anawamvera chisoni,+ chifukwa anali onyukanyuka ndi otayika ngati nkhosa zopanda m’busa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena