Ezekieli 34:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pang’ono ndi pang’ono zinamwazikana chifukwa chakuti zinalibe m’busa.+ Choncho zinakhala chakudya cha zilombo zonse zakutchire ndipo zinapitiriza kumwazikana.+
5 Pang’ono ndi pang’ono zinamwazikana chifukwa chakuti zinalibe m’busa.+ Choncho zinakhala chakudya cha zilombo zonse zakutchire ndipo zinapitiriza kumwazikana.+