Yesaya 56:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu nyama zonse zakutchire, inu nyama zonse za m’nkhalango, bwerani mudzadye.+ Yeremiya 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Tsoka abusa amene akuwononga ndi kubalalitsa nkhosa za pamalo anga odyetsera ziweto!”+ watero Yehova.
23 “Tsoka abusa amene akuwononga ndi kubalalitsa nkhosa za pamalo anga odyetsera ziweto!”+ watero Yehova.