Yeremiya 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Tsoka abusa amene akuwononga ndi kubalalitsa nkhosa zapamalo anga odyetsera ziweto!” akutero Yehova.+
23 “Tsoka abusa amene akuwononga ndi kubalalitsa nkhosa zapamalo anga odyetsera ziweto!” akutero Yehova.+