Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 10:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Abusa achita zinthu mopanda nzeru,+

      Ndipo sanafunse malangizo kwa Yehova.+

      Nʼchifukwa chake sanachite zinthu mozindikira,

      Ndipo ziweto zawo zonse zabalalika.”+

  • Yeremiya 50:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anthu anga akhala ngati gulu la nkhosa zosochera.+ Abusa awo ndi amene anawasocheretsa.+ Anawatenga nʼkupita nawo mʼmapiri ndipo ankangowayendetsa kuchoka paphiri kupita pachitunda. Iwo aiwala malo awo opumulirako.

  • Ezekieli 34:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Iwe mwana wa munthu, losera zoipa zimene zidzachitikire abusa a Isiraeli. Losera ndipo uuze abusawo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Tsoka abusa a Isiraeli,+ amene akhala akungodzidyetsa okha! Kodi abusa ntchito yawo si kudyetsa nkhosa?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena