1 Mafumu 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ahabu atangomuona Eliya, anati: “Ndiwe eti! Iwe ndiwe munthu amene wachititsa kuti Isiraeli anyanyalidwe.”+ 1 Mafumu 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Ahabu anafunsa Eliya kuti: “Wandipeza kodi mdani wanga?”+ Eliya anayankha kuti: “Inde ndakupezani. ‘Popeza watsimikiza mtima kuti uchite zoipa pamaso pa Yehova,+ Salimo 34:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Masoka adzapha munthu woipa.+Ndipo wodana ndi munthu wolungama adzapezeka wolakwa.+
17 Ahabu atangomuona Eliya, anati: “Ndiwe eti! Iwe ndiwe munthu amene wachititsa kuti Isiraeli anyanyalidwe.”+
20 Ndiyeno Ahabu anafunsa Eliya kuti: “Wandipeza kodi mdani wanga?”+ Eliya anayankha kuti: “Inde ndakupezani. ‘Popeza watsimikiza mtima kuti uchite zoipa pamaso pa Yehova,+