Luka 9:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Ophunzira ake, Yakobo ndi Yohane,+ ataona zimenezi anati: “Ambuye, kodi mukufuna tiwaitanire moto+ kuchokera kumwamba kuti uwanyeketse?”
54 Ophunzira ake, Yakobo ndi Yohane,+ ataona zimenezi anati: “Ambuye, kodi mukufuna tiwaitanire moto+ kuchokera kumwamba kuti uwanyeketse?”