Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 26:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Kenako Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa ndi kundisiya ndekha usiku uno, pakuti Malemba amati, ‘Ndidzapha m’busa, ndipo nkhosa za m’gululo zidzabalalika.’+

  • Mateyu 26:67
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 67 Kenako anayamba kumulavulira kunkhope+ ndi kum’menya+ nkhonya. Ena anamuwomba mbama,+

  • Mateyu 27:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Atatero anamulavulira+ ndi kutenga bango lija ndi kuyamba kum’menya nalo m’mutu.

  • Maliko 14:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Tsopano Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa kundisiya ndekha, chifukwa Malemba amati, ‘Ndidzapha m’busa,+ ndipo nkhosa zidzabalalika.’+

  • Yohane 18:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Atanena zimenezi, mmodzi wa alonda amene anaimirira chapafupi anamenya Yesu mbama,+ ndi kunena kuti: “Ungamuyankhe choncho wansembe wamkulu?”

  • Yohane 19:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pamenepo anayamba kubwera kwa iye ndi kunena kuti: “Mtendere ukhale nanu, inu Mfumu ya Ayuda!” Komanso anali kumumenya mapama.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena