Mateyu 27:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 n’kumanena kuti: “Iwe wogwetsa kachisi+ ndi kum’manga m’masiku atatu, dzipulumutse! Ngati ulidi mwana wa Mulungu, tsikatu pamtengo wozunzikirapowo!”+ Maliko 14:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 “Ife tinamva iyeyu akunena kuti, ‘Ine ndidzagwetsa kachisi uyu amene anamangidwa ndi manja, ndipo m’masiku atatu okha ndidzamanga wina osati womangidwa ndi manja.’”+
40 n’kumanena kuti: “Iwe wogwetsa kachisi+ ndi kum’manga m’masiku atatu, dzipulumutse! Ngati ulidi mwana wa Mulungu, tsikatu pamtengo wozunzikirapowo!”+
58 “Ife tinamva iyeyu akunena kuti, ‘Ine ndidzagwetsa kachisi uyu amene anamangidwa ndi manja, ndipo m’masiku atatu okha ndidzamanga wina osati womangidwa ndi manja.’”+