1 Mafumu 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Kodi waona mmene Ahabu wadzichepetsera pamaso panga?+ Popeza wadzichepetsa chifukwa cha ine, sindidzabweretsa tsokali m’masiku ake.+ M’malomwake, ndidzalibweretsa panyumba yake m’masiku a mwana wake.”+ 1 Mbiri 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kumbukirani ntchito zodabwitsa zimene wachita,+Kumbukirani zozizwitsa zake ndi zigamulo zotuluka m’kamwa mwake,+
29 “Kodi waona mmene Ahabu wadzichepetsera pamaso panga?+ Popeza wadzichepetsa chifukwa cha ine, sindidzabweretsa tsokali m’masiku ake.+ M’malomwake, ndidzalibweretsa panyumba yake m’masiku a mwana wake.”+
12 Kumbukirani ntchito zodabwitsa zimene wachita,+Kumbukirani zozizwitsa zake ndi zigamulo zotuluka m’kamwa mwake,+