Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Usaziweramire kapena kuzitumikira,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha,*+ wolanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo, chifukwa cha zolakwa za abambo a anthu odana ndi ine.+

  • 2 Mafumu 9:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Kenako Yehu anauza msilikali wake womuthandiza pagaleta+ dzina lake Bidikara, kuti: “Munyamule, umuponye m’munda wa Naboti Myezereeli.+ Kumbukira kuti iwe ndi ine tinkayenda pambuyo pa Ahabu bambo ake, aliyense atakwera pagaleta lake la mahatchi awiri, pa nthawi imene Yehova anam’temberera+ kuti:

  • 2 Mafumu 10:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Anthuwo atangolandira kalatayo, anatenga ana aamuna a mfumu okwanira 70 aja+ n’kuwapha. Kenako anatenga mitu yawo n’kuiika m’madengu, ndipo anaitumiza kwa Yehu ku Yezereeli.

  • 2 Mafumu 10:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kuwonjezera apo, Yehu anapitiriza kupha onse a m’nyumba ya Ahabu amene anatsala ku Yezereeli, amuna ake onse olemekezeka,+ anzake, ndi ansembe ake,+ mpaka onse anatha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena