5 Atatero anapita kunyumba ya bambo ake ku Ofira+ ndi kupha abale ake,+ ana aamuna 70 a Yerubaala, pamwala umodzi. Koma sanaphe Yotamu, mwana wamng’ono kwambiri mwa ana aamuna a Yerubaala, chifukwa anali atabisala.
21 ndikubweretsera tsoka+ ndipo ndithu ndidzaseseratu nyumba yako,+ ndi kupha munthu aliyense wokodzera khoma+ wa m’banja la Ahabu, ngakhale anthu onyozeka ndi opanda pake mu Isiraeli.